Ekisodo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitatero Mose anavomereza kukhala ndi Reueli, ndipo iye anapereka Zipora+ mwana wake wamkazi kwa Mose. Ekisodo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Mose anakhala m’busa wa ziweto za Yetero,*+ wansembe wa ku Midiyani, amene anali apongozi ake.+ Pamene anali kuweta ziwetozo chakumadzulo kwa chipululu, anafika kuphiri la Mulungu woona,+ ku Horebe.+
21 Zitatero Mose anavomereza kukhala ndi Reueli, ndipo iye anapereka Zipora+ mwana wake wamkazi kwa Mose.
3 Tsopano Mose anakhala m’busa wa ziweto za Yetero,*+ wansembe wa ku Midiyani, amene anali apongozi ake.+ Pamene anali kuweta ziwetozo chakumadzulo kwa chipululu, anafika kuphiri la Mulungu woona,+ ku Horebe.+