16 Ndiyeno wansembe+ wa ku Midiyani anali ndi ana aakazi 7. Monga mwa masiku onse, iwo anafika pachitsimepo ndipo anatunga madzi ndi kuwathira m’ngalande kuti ziweto za bambo awo zimwe.+
18Tsopano Yetero, wansembe wa ku Midiyani, apongozi ake a Mose,+ anamva zonse zimene Mulungu anachitira Mose ndi Aisiraeli, anthu a Mulungu, ndi mmene Yehova anawatulutsira ku Iguputo.+