Ekisodo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mose ndi Yoswa mtumiki wake ananyamuka, ndipo Mose anakwera m’phiri la Mulungu woona.+