Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inuyotu munanena kuti, ‘Mosakayikira m’pang’ono pomwe ndidzakusamalira, ndipo ndidzachulukitsa mbewu yako ngati mchenga wa kunyanja, umene suwerengeka kuchuluka kwake.’”+

  • Ekisodo 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho nditsikira kwa iwo kuti ndiwalanditse m’manja mwa Aiguputo,+ ndi kuwatulutsa m’dzikolo, n’kuwalowetsa m’dziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi.+

  • Ekisodo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+

  • Numeri 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+

      Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+

      Kodi ananenapo kanthu koma osachita,

      Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena