Rute 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atatero, Boazi anati: “Yehova akudalitse,+ mwana wanga. Kukoma mtima kosatha+ kumene wasonyeza panopa kukuposa koyamba kuja,+ popeza sunafune anyamata, kaya osauka kapena olemera.
10 Atatero, Boazi anati: “Yehova akudalitse,+ mwana wanga. Kukoma mtima kosatha+ kumene wasonyeza panopa kukuposa koyamba kuja,+ popeza sunafune anyamata, kaya osauka kapena olemera.