Rute 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atatero Naomi anauza mpongozi wakeyo kuti: “Yehova amene sanaleke kusonyeza chikondi chokhulupirika kwa amoyo ndi akufa, amudalitse munthu ameneyu.”+ Ndipo Naomi anapitiriza kuti: “Munthuyutu ndi wachibale wathu.+ Ndi mmodzi wa otiwombola.”+ Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:20 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2021, ptsa. 12-13 Tsanzirani, ptsa. 43-45 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, ptsa. 20-21
20 Atatero Naomi anauza mpongozi wakeyo kuti: “Yehova amene sanaleke kusonyeza chikondi chokhulupirika kwa amoyo ndi akufa, amudalitse munthu ameneyu.”+ Ndipo Naomi anapitiriza kuti: “Munthuyutu ndi wachibale wathu.+ Ndi mmodzi wa otiwombola.”+
2:20 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2021, ptsa. 12-13 Tsanzirani, ptsa. 43-45 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, ptsa. 20-21