Genesis 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+ 1 Samueli 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano mwamuna wina wa fuko la Benjamini anathamanga kuchoka kumalo ankhondowo kukafika ku Silo tsiku limenelo, atang’amba zovala zake+ ndi kudzithira dothi kumutu.+
34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+
12 Tsopano mwamuna wina wa fuko la Benjamini anathamanga kuchoka kumalo ankhondowo kukafika ku Silo tsiku limenelo, atang’amba zovala zake+ ndi kudzithira dothi kumutu.+