Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yoswa ataona zimenezi anang’amba malaya ake. Kenako anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi+ patsogolo pa likasa la Yehova, mpaka madzulo. Anachita zimenezi pamodzi ndi akulu a Isiraeli, n’kumadzithira fumbi kumutu kwawo.+

  • 2 Samueli 13:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako Tamara anadzithira phulusa+ kumutu ndi kung’amba malaya ake amizeremizere aja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu+ n’kunyamuka kumapita, akulira.

  • 2 Samueli 15:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ndiyeno pamene Davide anafika pamwamba pa phiri pamene anthu anali kugwadira Mulungu, anaona Husai+ Mwareki+ akubwera kudzakumana naye, atang’amba chovala chake ndiponso atadzithira dothi kumutu.+

  • Nehemiya 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu.

  • Yobu 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Atakweza maso awo ali chapatali, sanamuzindikire poyamba. Kenako anayamba kulira mokweza mawu ndipo aliyense anang’amba+ malaya ake akunja odula manja, n’kuwaza fumbi m’mwamba pamwamba pa mitu yawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena