Nehemiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu. Maliro 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+Iwo athira fumbi pamitu+ yawo ndipo avala ziguduli.*+Anamwali a Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka padothi.+ Ezekieli 27:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iwo adzakulirira mofuula ndi mowawidwa mtima.+ Adzadzithira dothi kumutu+ ndi kugubuduzika paphulusa.+
9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu.
10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+Iwo athira fumbi pamitu+ yawo ndipo avala ziguduli.*+Anamwali a Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka padothi.+
30 Iwo adzakulirira mofuula ndi mowawidwa mtima.+ Adzadzithira dothi kumutu+ ndi kugubuduzika paphulusa.+