Ezekieli 27:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iwo adzafuula ndipo adzakulirira mopwetekedwa mtima+Uku akudzithira dothi kumutu kwawo komanso kudzigubuduza paphulusa.
30 Iwo adzafuula ndipo adzakulirira mopwetekedwa mtima+Uku akudzithira dothi kumutu kwawo komanso kudzigubuduza paphulusa.