Yesaya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uwu ndi uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,+ Chifukwa chakuti doko lawonongedwa ndipo simungathenso kufikapo. Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+ Ezekieli 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo adzakuimbira nyimbo yoimba polira.+ Azidzati: “Iwe mzinda wotamandika, zoona wawonongekadi!+ Mwa iwe munkakhala anthu ochokera kunyanja.Iwe ndi anthu ako munali amphamvu panyanja,+Munkachititsa mantha anthu onse okhala padziko lapansi.
23 Uwu ndi uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,+ Chifukwa chakuti doko lawonongedwa ndipo simungathenso kufikapo. Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+
17 Iwo adzakuimbira nyimbo yoimba polira.+ Azidzati: “Iwe mzinda wotamandika, zoona wawonongekadi!+ Mwa iwe munkakhala anthu ochokera kunyanja.Iwe ndi anthu ako munali amphamvu panyanja,+Munkachititsa mantha anthu onse okhala padziko lapansi.