Genesis 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana a Yafeti anali Gomeri,+ Magogi,+ Madai, Yavani, Tubala,+ Meseki+ ndi Tirasi.+ Genesis 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Yavani anali Elisha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu. Yeremiya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Koma wolokerani kuzilumba za ku Kitimu+ kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwinoNʼkuona ngati zoterezi zinayamba zachitikapo kumeneko. Ezekieli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zopalasira zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana,Ndipo mbali yakutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, nʼkuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+
10 ‘Koma wolokerani kuzilumba za ku Kitimu+ kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwinoNʼkuona ngati zoterezi zinayamba zachitikapo kumeneko.
6 Zopalasira zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana,Ndipo mbali yakutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, nʼkuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+