Ezekieli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zopalasira ngalawa zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana. Mbali ya kutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, n’kuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:6 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, tsa. 17
6 Zopalasira ngalawa zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana. Mbali ya kutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, n’kuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+