Ezekieli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zopalasira zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana,Ndipo mbali yakutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, nʼkuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:6 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, tsa. 17
6 Zopalasira zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana,Ndipo mbali yakutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, nʼkuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+