Genesis 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.+ Yesaya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+ Yeremiya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Wolokerani ku Kitimu,+ m’mbali mwa nyanja, kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwino kuti muone ngati zoterezi zinachitikapo kumeneko.+
23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+
10 “‘Wolokerani ku Kitimu,+ m’mbali mwa nyanja, kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwino kuti muone ngati zoterezi zinachitikapo kumeneko.+