Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.+

  • Yeremiya 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Wolokerani ku Kitimu,+ m’mbali mwa nyanja, kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwino kuti muone ngati zoterezi zinachitikapo kumeneko.+

  • Ezekieli 27:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zopalasira ngalawa zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana. Mbali ya kutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, n’kuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+

  • Danieli 11:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Choncho zombo za ku Kitimu+ zidzabwera ndi kumuukira ndipo adzakhala wachisoni.

      “Iye adzabwerera ndi kulankhula mawu amphamvu odzudzula+ pangano lopatulika+ ndipo adzachita zofuna zake. Pamenepo iye adzabwerera ndi kuganizira anthu osiya pangano lopatulika.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena