Genesis 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+ Salimo 120:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+ Yeremiya 49:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ponena za Kedara+ ndi maufumu a Hazori+ amene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anawapha,+ Yehova wanena kuti: “Nyamukani amuna inu, pitani ku Kedara ndipo mukafunkhe zinthu za ana a Kum’mawa.+
13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+
5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+
28 Ponena za Kedara+ ndi maufumu a Hazori+ amene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anawapha,+ Yehova wanena kuti: “Nyamukani amuna inu, pitani ku Kedara ndipo mukafunkhe zinthu za ana a Kum’mawa.+