Yeremiya 49:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Hazori+ adzakhala malo obisalamo mimbulu+ ndipo adzakhala bwinja mpaka kalekale. Palibe munthu amene adzakhala kumeneko, moti mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo.”+
33 “Hazori+ adzakhala malo obisalamo mimbulu+ ndipo adzakhala bwinja mpaka kalekale. Palibe munthu amene adzakhala kumeneko, moti mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo.”+