Yeremiya 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa m’manja mwa mtumiki wanga+ Nebukadinezara, mfumu ya Babulo.+ Ndamupatsanso nyama zakutchire kuti zimutumikire.+
6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa m’manja mwa mtumiki wanga+ Nebukadinezara, mfumu ya Babulo.+ Ndamupatsanso nyama zakutchire kuti zimutumikire.+