14 Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Ndidzaika magoli achitsulo pamakosi a mitundu ya anthu yonseyi kuti atumikire Nebukadinezara mfumu ya Babulo,+ ndipo ndikunenetsa kuti adzamutumikiradi.+ Nebukadinezara ndidzamupatsanso ngakhale nyama zakutchire.”’”+