Genesis 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.+ Numeri 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Padzafika zombo zochokera kugombe la Kitimu,+Ndipo iwo adzasautsa Asuri+ ndithu,Adzasautsadi Ebere.Koma iyenso adzawonongeka pamapeto pake.”
24 Padzafika zombo zochokera kugombe la Kitimu,+Ndipo iwo adzasautsa Asuri+ ndithu,Adzasautsadi Ebere.Koma iyenso adzawonongeka pamapeto pake.”