Nahumu 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Uwu ndi uthenga wokhudza Nineve:+ Buku la masomphenya a Nahumu wa ku Elikosi: Nahumu 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Abusa ako ayamba kuwodzera,+ iwe mfumu ya Asuri, ndipo anthu ako olemekezeka akungokhala m’nyumba zawo.+ Anthu ako amwazikana pamapiri ndipo palibe amene akuwasonkhanitsa pamodzi.+
18 “Abusa ako ayamba kuwodzera,+ iwe mfumu ya Asuri, ndipo anthu ako olemekezeka akungokhala m’nyumba zawo.+ Anthu ako amwazikana pamapiri ndipo palibe amene akuwasonkhanitsa pamodzi.+