1 Mafumu 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika+ m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri. Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+ Nahumu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchokera pamene Nineve anakhalapo,+ iye wakhala ngati dziwe la madzi,+ koma tsopano anthu ake akuthawa. Ena akufuula kuti: “Imani amuna inu! Imani!” Koma palibe amene akubwerera.+ Chivumbulutso 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mafumu a dziko lapansi, nduna, akuluakulu a asilikali, olemera, amphamvu, kapolo aliyense ndi mfulu aliyense, anabisala m’mapanga ndi m’matanthwe+ a m’mapiri.
17 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika+ m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri. Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+
8 Kuchokera pamene Nineve anakhalapo,+ iye wakhala ngati dziwe la madzi,+ koma tsopano anthu ake akuthawa. Ena akufuula kuti: “Imani amuna inu! Imani!” Koma palibe amene akubwerera.+
15 Mafumu a dziko lapansi, nduna, akuluakulu a asilikali, olemera, amphamvu, kapolo aliyense ndi mfulu aliyense, anabisala m’mapanga ndi m’matanthwe+ a m’mapiri.