Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Chinthu choopsa kwa woipa n’chimene chidzamubwerere,+ koma anthu olungama adzapatsidwa zimene amalakalaka.+

  • Zekariya 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Aterafi*+ amalankhula zoipa. Ochita zamaula amaona masomphenya onama+ ndipo amafotokoza maloto opanda pake. Iwo saphula kanthu polimbikitsa anthu.+ N’chifukwa chake adzasochere ngati nkhosa.+ Iwo adzavutika chifukwa adzakhala opanda m’busa.+

  • Zekariya 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Iwe lupanga, nyamuka ukanthe m’busa wanga.+ Ukanthe mwamuna wamphamvu yemwe ndi mnzanga,”+ watero Yehova wa makamu. “Ipha m’busa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+ Ine ndidzakomera mtima nkhosa zonyozeka.”+

  • Mateyu 9:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Poona chikhamu cha anthu, iye anawamvera chisoni,+ chifukwa anali onyukanyuka ndi otayika ngati nkhosa zopanda m’busa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena