Salimo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwaipatsa zokhumba za mtima wake,+Ndipo simunaimane zokhumba za pakamwa pake.+ [Seʹlah.] Salimo 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso sangalala mwa Yehova,+Ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako.+ Yohane 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kufikira nthawi ino simunapemphepo chilichonse m’dzina langa. Pemphani ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chisefukire.+ 1 Yohane 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+
24 Kufikira nthawi ino simunapemphepo chilichonse m’dzina langa. Pemphani ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chisefukire.+
14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+