2 Mbiri 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+ Ezekieli 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iweyo ukachenjeza munthu woipa kuti asiye njira zake ndi kubwerera, koma iye osasiya njira zake zoipa ndi kubwerera, munthuyo adzafa chifukwa cha zoipa zake.+ Koma iweyo udzapulumutsa moyo wako.+
16 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+
9 Koma iweyo ukachenjeza munthu woipa kuti asiye njira zake ndi kubwerera, koma iye osasiya njira zake zoipa ndi kubwerera, munthuyo adzafa chifukwa cha zoipa zake.+ Koma iweyo udzapulumutsa moyo wako.+