Miyambo 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wosiya njira yabwino amadana ndi malangizo.+ Aliyense wodana ndi chidzudzulo adzafa.+