Yesaya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Yehova akadzatsiriza ntchito yake yonse m’phiri la Ziyoni ndi mu Yerusalemu, ndidzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha zipatso za mwano wa mumtima mwake ndiponso chifukwa cha kudzikuza kwa maso ake onyada.+ Nahumu 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense wokuona adzakuthawa+ ndipo adzanena kuti, ‘Nineve wasakazidwa! Ndani adzamuchitira chisoni?’ Kodi anthu oti akutonthoze ndiwapeza kuti? Zefaniya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iye adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.+ Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko lopanda madzi ngati chipululu.
12 “Yehova akadzatsiriza ntchito yake yonse m’phiri la Ziyoni ndi mu Yerusalemu, ndidzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha zipatso za mwano wa mumtima mwake ndiponso chifukwa cha kudzikuza kwa maso ake onyada.+
7 Aliyense wokuona adzakuthawa+ ndipo adzanena kuti, ‘Nineve wasakazidwa! Ndani adzamuchitira chisoni?’ Kodi anthu oti akutonthoze ndiwapeza kuti?
13 “Iye adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.+ Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko lopanda madzi ngati chipululu.