2 Mafumu 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Rabisake+ anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+ 2 Mafumu 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+ Salimo 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa anthu osautsika mudzawapulumutsa,+Koma anthu odzikweza mudzawatsitsa.+
19 Choncho Rabisake+ anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+
35 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+