Yesaya 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Rabisake anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri+ yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+
4 Choncho Rabisake anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri+ yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+