2 Mafumu 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukum’dalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu+ saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+ Salimo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu ana a anthu, kodi mudzandinyoza chifukwa cha ulemerero wanga+ kufikira liti?Mudzakonda zinthu zopanda pake kufikira liti?Mudzafunafuna nkhani yoti mundinamizire kufikira liti? [Seʹlah.] Yesaya 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukumudalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukum’dalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu+ saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
2 Inu ana a anthu, kodi mudzandinyoza chifukwa cha ulemerero wanga+ kufikira liti?Mudzakonda zinthu zopanda pake kufikira liti?Mudzafunafuna nkhani yoti mundinamizire kufikira liti? [Seʹlah.]
10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukumudalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+