Yobu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mutu wanga ukadzikweza,+ mudzandisaka ngati kuti ndinu mkango wamphamvu,+Ndipo mudzandichitira chinthu chinanso chodabwitsa. Yobu 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mkwiyo wako wosefukira utuluke,+Ndipo uone aliyense wodzikweza n’kumutsitsa. Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+ Yesaya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maso odzikuza a munthu wochokera kufumbi adzatsika, ndipo anthu odzikweza adzawerama.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+ Luka 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndithu ndikukuuzani, Munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kukhala wolungama kwambiri+ kusiyana ndi wina uja, chifukwa aliyense wodzikweza adzam’nyazitsa, koma wodzichepetsa adzamukweza.”+
16 Mutu wanga ukadzikweza,+ mudzandisaka ngati kuti ndinu mkango wamphamvu,+Ndipo mudzandichitira chinthu chinanso chodabwitsa.
11 Maso odzikuza a munthu wochokera kufumbi adzatsika, ndipo anthu odzikweza adzawerama.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+
14 Ndithu ndikukuuzani, Munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kukhala wolungama kwambiri+ kusiyana ndi wina uja, chifukwa aliyense wodzikweza adzam’nyazitsa, koma wodzichepetsa adzamukweza.”+