Salimo 78:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anawasonyeza mkwiyo wake woyaka moto,+Ukali, ziweruzo zamphamvu ndi masautso.+Anawatumizira makamu a angelo obweretsa masoka.+ Salimo 90:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndani angadziwe kukula kwa ukali wanu,+Ndi kukula kwa mkwiyo wanu kumene kumafanana ndi ulemu umene muyenera kulandira?+ Yeremiya 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Taonani! Mphepo yamkuntho yochokera kwa Yehova yawomba. Mkwiyo wake wawomba ngati kamvulumvulu wosakaza.+ Wawomba pamitu ya anthu oipa.+
49 Anawasonyeza mkwiyo wake woyaka moto,+Ukali, ziweruzo zamphamvu ndi masautso.+Anawatumizira makamu a angelo obweretsa masoka.+
11 Ndani angadziwe kukula kwa ukali wanu,+Ndi kukula kwa mkwiyo wanu kumene kumafanana ndi ulemu umene muyenera kulandira?+
23 Taonani! Mphepo yamkuntho yochokera kwa Yehova yawomba. Mkwiyo wake wawomba ngati kamvulumvulu wosakaza.+ Wawomba pamitu ya anthu oipa.+