Oweruza 9:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndipo zoipa zonse za amuna a m’Sekemu, Mulungu anachititsa kuti ziwabwerere pamutu pawo, kuti temberero+ la Yotamu+ mwana wa Yerubaala,+ liwagwere.+ Miyambo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova anapanga chilichonse n’cholinga,+ ndipo ngakhale woipa anamusungira tsiku loipa.+
57 Ndipo zoipa zonse za amuna a m’Sekemu, Mulungu anachititsa kuti ziwabwerere pamutu pawo, kuti temberero+ la Yotamu+ mwana wa Yerubaala,+ liwagwere.+