Salimo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+ Yesaya 42:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Mulungu anali kuwakhuthulira mkwiyo, ukali wake, ndi nkhondo yoopsa.+ Nkhondoyo inali kuwapsereza+ koma iwo sanazindikire.+ Inapitiriza kuwatentha koma iwo sanaganizire chilichonse mumtima mwawo.+
6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+
25 Choncho Mulungu anali kuwakhuthulira mkwiyo, ukali wake, ndi nkhondo yoopsa.+ Nkhondoyo inali kuwapsereza+ koma iwo sanazindikire.+ Inapitiriza kuwatentha koma iwo sanaganizire chilichonse mumtima mwawo.+