Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukum’dalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu+ saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+

  • 2 Mbiri 32:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Senakeribu mfumu ya Asuri yanena kuti,+ ‘Kodi mukudalira chiyani poti mukungokhala mosatekeseka, Yerusalemu atazunguliridwa?+

  • Salimo 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu ana a anthu, kodi mudzandinyoza chifukwa cha ulemerero wanga+ kufikira liti?

      Mudzakonda zinthu zopanda pake kufikira liti?

      Mudzafunafuna nkhani yoti mundinamizire kufikira liti? [Seʹlah.]

  • Yesaya 36:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ngati inu mungandiuze kuti, ‘Tikudalira Yehova Mulungu wathu,’ kodi si iye amene Hezekiya wamuchotsera malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe,+ n’kuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada pamaso pa guwa lansembe ili’?”’+

  • Yesaya 37:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukumudalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena