Salimo 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+ Yesaya 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Rabisake anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri+ yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+
39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+
4 Choncho Rabisake anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri+ yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+