Yesaya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akadzamaliza ntchito yake yonse mʼphiri la Ziyoni komanso mu Yerusalemu, adzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha mwano umene uli mumtima mwake ndiponso chifukwa chakuti amayangʼana monyada ndi modzikuza.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:12 Galamukani!,12/2010, tsa. 28 Yesaya 1, ptsa. 147-148
12 Yehova akadzamaliza ntchito yake yonse mʼphiri la Ziyoni komanso mu Yerusalemu, adzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha mwano umene uli mumtima mwake ndiponso chifukwa chakuti amayangʼana monyada ndi modzikuza.+