Yesaya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uwu ndi uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,+ Chifukwa chakuti doko lawonongedwa ndipo simungathenso kufikapo. Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:1 Yesaya 1, ptsa. 244-245
23 Uwu ndi uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,+ Chifukwa chakuti doko lawonongedwa ndipo simungathenso kufikapo. Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+