Yesaya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:1 Yesaya 1, ptsa. 244-245
23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+