2 Mbiri 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 pakuti zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide, siliva,+ minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.+ Salimo 48:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pogwiritsa ntchito mphepo yamphamvu ya kum’mawa, munaswa zombo za ku Tarisi.+ Yesaya 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Lidzafikira zombo zonse za ku Tarisi,+ ndi ngalawa zonse zabwinozabwino. Ezekieli 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘“Zombo za ku Tarisi+ zoyenda m’gulu limodzi zinali kunyamula katundu wako wamalonda. Choncho unalemera ndi kukhala waulemerero kwambiri pakati pa nyanja.+
21 pakuti zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide, siliva,+ minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.+
25 “‘“Zombo za ku Tarisi+ zoyenda m’gulu limodzi zinali kunyamula katundu wako wamalonda. Choncho unalemera ndi kukhala waulemerero kwambiri pakati pa nyanja.+