1 Mafumu 22:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehosafati anapanga zombo za ku Tarisi+ kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide, koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+ Yesaya 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Lidzafikira zombo zonse za ku Tarisi,+ ndi ngalawa zonse zabwinozabwino. Yeremiya 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzawamwaza pamaso pa adani awo ngati mmene mphepo yochokera kum’mawa imamwazira fumbi.+ Sindidzawaonetsa nkhope yanga,+ koma ndidzawafulatira pa tsiku la tsoka lawo.” Ezekieli 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘“Anthu okupalasa akupititsa pamadzi ozama.+ Mphepo ya kum’mawa yakuwononga pakatikati pa nyanja.+
48 Yehosafati anapanga zombo za ku Tarisi+ kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide, koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+
17 Ndidzawamwaza pamaso pa adani awo ngati mmene mphepo yochokera kum’mawa imamwazira fumbi.+ Sindidzawaonetsa nkhope yanga,+ koma ndidzawafulatira pa tsiku la tsoka lawo.”
26 “‘“Anthu okupalasa akupititsa pamadzi ozama.+ Mphepo ya kum’mawa yakuwononga pakatikati pa nyanja.+