1 Mafumu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+ 2 Mbiri 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Eliezere mwana wa Dodavahu wa ku Maresa analankhula mwaulosi motsutsana ndi Yehosafati, kuti: “Popeza mwachita mgwirizano ndi Ahaziya,+ Yehova awononga ntchito zanu.”+ Chotero zombozo zinasweka+ ndipo sizinathenso kupita ku Tarisi.+
26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+
37 Koma Eliezere mwana wa Dodavahu wa ku Maresa analankhula mwaulosi motsutsana ndi Yehosafati, kuti: “Popeza mwachita mgwirizano ndi Ahaziya,+ Yehova awononga ntchito zanu.”+ Chotero zombozo zinasweka+ ndipo sizinathenso kupita ku Tarisi.+