Numeri 33:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako ananyamuka ku Abirona n’kukamanga msasa ku Ezioni-geberi.+ Deuteronomo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+ “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+ 1 Mafumu 22:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehosafati anapanga zombo za ku Tarisi+ kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide, koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+
8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+ “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+
48 Yehosafati anapanga zombo za ku Tarisi+ kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide, koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+