Deuteronomo 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Si paja mapiri amenewa ali kuchigawo chotulukira dzuwa cha Yorodano, m’dziko la Akanani okhala mu Araba,+ moyang’anizana ndi Giligala,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya ku More?+
30 Si paja mapiri amenewa ali kuchigawo chotulukira dzuwa cha Yorodano, m’dziko la Akanani okhala mu Araba,+ moyang’anizana ndi Giligala,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya ku More?+