Deuteronomo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+ “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+ 1 Mafumu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+ 2 Mbiri 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapita ku Ezioni-geberi+ ndi ku Eloti,+ kugombe la nyanja m’dziko la Edomu.+
8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+ “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+
26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+
17 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapita ku Ezioni-geberi+ ndi ku Eloti,+ kugombe la nyanja m’dziko la Edomu.+