Numeri 33:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako ananyamuka ku Abirona n’kukamanga msasa ku Ezioni-geberi.+ 1 Mafumu 22:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehosafati anapanga zombo za ku Tarisi+ kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide, koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+ 2 Mbiri 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Chotero anayamba kugwira naye limodzi ntchito yopanga zombo zopita ku Tarisi.+ Zombozo anazipangira ku Ezioni-geberi.+
48 Yehosafati anapanga zombo za ku Tarisi+ kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide, koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+
36 Chotero anayamba kugwira naye limodzi ntchito yopanga zombo zopita ku Tarisi.+ Zombozo anazipangira ku Ezioni-geberi.+