1 Mafumu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide,+ siliva, minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko. 1 Mafumu 22:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehosafati anapanga zombo za ku Tarisi+ kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide, koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+
22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide,+ siliva, minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.
48 Yehosafati anapanga zombo za ku Tarisi+ kuti zizipita ku Ofiri kukatenga golide, koma sizinapite chifukwa zinasweka ku Ezioni-geberi.+