1 Mafumu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Itatero, mfumuyo inapanga mpando wachifumu+ waukulu waminyanga ya njovu,+ n’kuukuta ndi golide woyenga bwino.+ Amosi 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nyumba yokhalamo m’nyengo yozizira+ ndi nyumba yokhalamo m’nyengo yotentha+ ndidzazigwetsa.’ “‘Nyumba zaminyanga ya njovu zidzafafanizidwa+ ndipo nyumba zambiri zidzawonongedwa,’+ watero Yehova.”
18 Itatero, mfumuyo inapanga mpando wachifumu+ waukulu waminyanga ya njovu,+ n’kuukuta ndi golide woyenga bwino.+
15 Nyumba yokhalamo m’nyengo yozizira+ ndi nyumba yokhalamo m’nyengo yotentha+ ndidzazigwetsa.’ “‘Nyumba zaminyanga ya njovu zidzafafanizidwa+ ndipo nyumba zambiri zidzawonongedwa,’+ watero Yehova.”