Yesaya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndamva Yehova wa makamu akulumbira kuti nyumba zambiri, ngakhale zitakhala zikuluzikulu ndiponso zabwino, zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiri ndipo zidzakhala zopanda wokhalamo.+ Amosi 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Tsopano Yehova akalamula,+ nyumba zikuluzikulu zigwetsedwa n’kusanduka mulu wa dothi ndipo nyumba zing’onozing’ono zisanduka zibuma zokhazokha.+
9 Ndamva Yehova wa makamu akulumbira kuti nyumba zambiri, ngakhale zitakhala zikuluzikulu ndiponso zabwino, zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiri ndipo zidzakhala zopanda wokhalamo.+
11 “‘Tsopano Yehova akalamula,+ nyumba zikuluzikulu zigwetsedwa n’kusanduka mulu wa dothi ndipo nyumba zing’onozing’ono zisanduka zibuma zokhazokha.+